Ekisodo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Aroni anayankha kuti: “Mkwiyo wa mbuyanga usayake. Inuyo mukuwadziwa bwino anthuwa, kuti amakonda kuchita zoipa.+ 1 Samueli 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Poyankha Sauli anati: “Anthuwa+ azitenga kwa Aamaleki, chifukwa sanaphe nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambirizi n’cholinga chofuna kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+ Koma zina zonse zotsala taziwononga.”
22 Ndipo Aroni anayankha kuti: “Mkwiyo wa mbuyanga usayake. Inuyo mukuwadziwa bwino anthuwa, kuti amakonda kuchita zoipa.+
15 Poyankha Sauli anati: “Anthuwa+ azitenga kwa Aamaleki, chifukwa sanaphe nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambirizi n’cholinga chofuna kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+ Koma zina zonse zotsala taziwononga.”