Deuteronomo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muwononge anthu a mitundu yonse amene Yehova Mulungu wanu akuwapereka kwa inu.+ Musawamvere chisoni+ ndipo musatumikire milungu yawo+ chifukwa kuchita zimenezo kudzakutcherani msampha.+ 1 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+
16 Muwononge anthu a mitundu yonse amene Yehova Mulungu wanu akuwapereka kwa inu.+ Musawamvere chisoni+ ndipo musatumikire milungu yawo+ chifukwa kuchita zimenezo kudzakutcherani msampha.+
3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+