12 Tsopano Davide anali mwana wamwamuna wa Jese, Mwefurata+ wina wa ku Betelehemu, ku Yuda. Jese anali ndi ana aamuna 8+ ndipo m’masiku a Sauli iye anali atakalamba kale.
6 Ngati bambo ako angafunse za ine, uwauze kuti, ‘Davide anandichonderera kuti ndimulole kuchoka kuti athamangire kumzinda wakwawo ku Betelehemu,+ chifukwa banja lawo lonse likukapereka nsembe ya pachaka.’+