1 Samueli 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Davide anapita kwa Sauli ndipo anali kum’tumikira.+ Sauli anam’konda kwambiri Davide, moti anakhala womunyamulira zida zake.+ 1 Samueli 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsiku limenelo Sauli anatenga Davide, ndipo sanamulole kubwerera kunyumba ya bambo ake.+ 1 Samueli 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero Sauli anachotsa Davide kuti asamakhale naye pafupi,+ ndipo anamuika kukhala mtsogoleri wa gulu la asilikali 1,000, moti Davide anali kutsogolera asilikali amenewo.+
21 Choncho Davide anapita kwa Sauli ndipo anali kum’tumikira.+ Sauli anam’konda kwambiri Davide, moti anakhala womunyamulira zida zake.+
13 Chotero Sauli anachotsa Davide kuti asamakhale naye pafupi,+ ndipo anamuika kukhala mtsogoleri wa gulu la asilikali 1,000, moti Davide anali kutsogolera asilikali amenewo.+