Genesis 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndine wosayenerera kukoma mtima kosatha ndi kukhulupirika konseku, kumene mwandionetsa ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo tsopano ndili ndi magulu awiriwa.+ Yoswa 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtundu wonse utangotha kuwoloka mtsinje wa Yorodano,+ Yehova anauza Yoswa kuti:
10 Ine ndine wosayenerera kukoma mtima kosatha ndi kukhulupirika konseku, kumene mwandionetsa ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo tsopano ndili ndi magulu awiriwa.+