Yobu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi khutu si paja limasiyanitsa mawu+Ngati mmene m’kamwa+ mumasiyanitsira kakomedwe ka chakudya? Mlaliki 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 zitseko zotulukira popita mumsewu zidzatsekedwa,+ phokoso la miyala yoperera ufa lidzayamba kumveka motsika,+ ndipo munthu azidzadzuka ndi kulira kwa mbalame, ndiponso ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mawu otsika.+
4 zitseko zotulukira popita mumsewu zidzatsekedwa,+ phokoso la miyala yoperera ufa lidzayamba kumveka motsika,+ ndipo munthu azidzadzuka ndi kulira kwa mbalame, ndiponso ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mawu otsika.+