2 Samueli 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuwonjezera apo, pamene Abisalomu anali kupereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ Mgilo,+ phungu wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Chiwembu+ chimenecho chinapitiriza kukula ndipo chiwerengero cha anthu amene anali kutsatira Abisalomu chinapitiriza kuwonjezeka.+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+ Agalatiya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,
12 Kuwonjezera apo, pamene Abisalomu anali kupereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ Mgilo,+ phungu wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Chiwembu+ chimenecho chinapitiriza kukula ndipo chiwerengero cha anthu amene anali kutsatira Abisalomu chinapitiriza kuwonjezeka.+
21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+
20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,