Salimo 97:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pake pakuyaka moto,+Ndipo ukupsereza adani ake onse omuzungulira.+ Yesaya 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali. Likubwera ndi mkwiyo woyaka+ ndiponso mitambo yolemera. Pamilomo yake padzaza mawu odzudzula ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+
27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali. Likubwera ndi mkwiyo woyaka+ ndiponso mitambo yolemera. Pamilomo yake padzaza mawu odzudzula ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+