Salimo 144:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, weramitsani kumwamba kuti mutsike.+Khudzani mapiri kuti afuke utsi.+ Yesaya 64:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Zikanakhalatu bwino mukanang’amba kumwamba, mukanatsika pansi pano,+ komanso mapiri akanagwedezeka chifukwa cha inu,+
64 Zikanakhalatu bwino mukanang’amba kumwamba, mukanatsika pansi pano,+ komanso mapiri akanagwedezeka chifukwa cha inu,+