Salimo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+ Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+
10 Iye anafika atakwera pakerubi wouluka.+Mulungu anali kuuluka mwaliwiro pamapiko a cholengedwa chauzimu.*+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+