Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+ Salimo 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa nthawi imeneyo adani anga adzabwerera pa tsiku limene ndidzaitana inu.+Ndikudziwa bwino kuti Mulungu ali kumbali yanga.+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
9 Pa nthawi imeneyo adani anga adzabwerera pa tsiku limene ndidzaitana inu.+Ndikudziwa bwino kuti Mulungu ali kumbali yanga.+