Salimo 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzakhalabe wopanda cholakwa pamaso pake,+Ndipo ndidzayesetsa kupewa kuchita cholakwa.+ Miyambo 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu wanzeru amachita mantha ndipo amapatuka pa choipa,+ koma wopusa amapsa mtima ndiponso amakhala wodzidalira.+
16 Munthu wanzeru amachita mantha ndipo amapatuka pa choipa,+ koma wopusa amapsa mtima ndiponso amakhala wodzidalira.+