Salimo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+Andibwezere mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti njira za munthu zili pamaso pa Yehova,+ ndipo iye amaonetsetsa njira zake zonse.+
24 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+Andibwezere mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.+