Salimo 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti inu Yehova mudzandiyatsira nyale yanga,+Mulungu wanga adzandiunikira mu mdima.+ Salimo 97:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwala kwaunikira wolungama,+Ndipo anthu owongoka mtima akusangalala.+ Mateyu 13:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+
43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+