Deuteronomo 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mbali mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso kuchokera kumzinda wa m’chigwa mpaka ku Giliyadi, panalibe mzinda womwe unali wa malinga aatali kwambiri kwa ife.+ Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife. Salimo 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti ndi thandizo lanu, ndingathamangitse gulu la achifwamba.+Ndi thandizo la Mulungu wanga ndingakwere khoma.+
36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mbali mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso kuchokera kumzinda wa m’chigwa mpaka ku Giliyadi, panalibe mzinda womwe unali wa malinga aatali kwambiri kwa ife.+ Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.
29 Pakuti ndi thandizo lanu, ndingathamangitse gulu la achifwamba.+Ndi thandizo la Mulungu wanga ndingakwere khoma.+