Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka. Salimo 119:140 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 140 Mawu anu ndi oyengeka kwambiri,+Ndipo ine mtumiki wanu ndimawakonda.+ Miyambo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu alionse a Mulungu ndi oyera.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka.