1 Samueli 17:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+ Salimo 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Inu mudzandiveka mphamvu kuti ndithe kumenya nkhondo.Mudzakomola ondiukira.+ Salimo 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi thandizo lanu tidzakankha adani athu.+M’dzina lanu tidzapondereza amene akutiukira.+ Salimo 144:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+
49 Pamenepo Davide anapisa dzanja m’chikwama chake ndi kutengamo mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya+ Mfilisiti uja pamphumi n’kuloweratu m’mutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+
2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+