Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova adzakuchititsa kukhala kumutu osati kumchira. Pamenepo udzangokhala pamwamba+ ndipo sudzakhala m’munsi, chifukwa ukumvera malamulo+ a Yehova Mulungu wako amene ndikukupatsa lero kuti uwasunge ndi kuwatsatira.

  • 2 Samueli 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Davide anapha Hadadezeri,+ mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake kumeneko.

  • Salimo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+

      Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+

  • Salimo 60:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+

      Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+

      Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena