Salimo 18:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Alendo adzatha mphamvu,Ndipo adzatuluka m’malo awo achitetezo akunjenjemera.+ Mika 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+ Adzatuluka m’malo awo obisalamo+ ngati zokwawa zapadziko lapansi ali ndi mantha. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akunjenjemera ndipo adzachita nanu mantha.”+
17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+ Adzatuluka m’malo awo obisalamo+ ngati zokwawa zapadziko lapansi ali ndi mantha. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akunjenjemera ndipo adzachita nanu mantha.”+