Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo adzanena kuti: “Inetu ndakhazika mfumu yanga+Pa Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”+ Salimo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+
21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+