Salimo 18:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+ Salimo 89:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndapeza Davide mtumiki wanga,+Ndipo ndamudzoza ndi mafuta anga opatulika.+
50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+