Zekariya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anaumitsa mtima wawo+ ngati mwala wolimba kwambiri kuti asamvere malamulo+ ndi mawu a Yehova wa makamu, amene anawatumizira mwa mzimu wake+ kudzera mwa aneneri akale.+ Choncho Yehova wa makamu anakwiya kwambiri.”+ Maliko 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwa mzimu woyera,+ Davideyo ananena kuti, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja kufikira nditaika adani ako kunsi kwa mapazi ako.”’+ 2 Timoteyo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+
12 Iwo anaumitsa mtima wawo+ ngati mwala wolimba kwambiri kuti asamvere malamulo+ ndi mawu a Yehova wa makamu, amene anawatumizira mwa mzimu wake+ kudzera mwa aneneri akale.+ Choncho Yehova wa makamu anakwiya kwambiri.”+
36 Mwa mzimu woyera,+ Davideyo ananena kuti, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja kufikira nditaika adani ako kunsi kwa mapazi ako.”’+
16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+