1 Mbiri 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa amuna atatuwo, iye anali wolemekezeka kwambiri kuposa awiri enawo, ndipo anakhala mtsogoleri wawo. Koma sanafanane+ ndi amuna atatu oyambirira aja.
21 Pa amuna atatuwo, iye anali wolemekezeka kwambiri kuposa awiri enawo, ndipo anakhala mtsogoleri wawo. Koma sanafanane+ ndi amuna atatu oyambirira aja.