2 Samueli 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna ena 30 aja, ndipo anali mtsogoleri wawo, komabe sanafanane ndi amuna atatu oyamba aja.+
19 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna ena 30 aja, ndipo anali mtsogoleri wawo, komabe sanafanane ndi amuna atatu oyamba aja.+