Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndi kotheka, khalani mwamtendere+ ndi anthu onse, monga mmene mungathere.