2 Timoteyo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+ Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+ Yakobo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+
24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+
14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+
18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+