-
2 Samueli 19:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 mwa kukonda anthu odana nanu ndi kudana ndi anthu okukondani. Lero mwasonyeza kuti akulu ndi atumiki alibe ntchito kwa inu, chifukwa ine ndikudziwa bwino kuti Abisalomu akanakhala ndi moyo koma ena tonsefe n’kufa, pamenepo zikanakhala bwino kwa inu.
-