1 Samueli 14:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wamkazi wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, m’bale wa bambo ake a Sauli. 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+ 2 Samueli 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero, Abineri anatumiza mithenga kwa Davide nthawi yomweyo, kuti akamuuze kuti: “Kodi mwini dziko ndani?” Ndiyeno anawonjezera kuti: “Chita nane pangano, ndipo inetu ndidzakuthandiza kutembenuza Isiraeli yense kukhala kumbali yako.”+
50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wamkazi wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, m’bale wa bambo ake a Sauli.
8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+
12 Chotero, Abineri anatumiza mithenga kwa Davide nthawi yomweyo, kuti akamuuze kuti: “Kodi mwini dziko ndani?” Ndiyeno anawonjezera kuti: “Chita nane pangano, ndipo inetu ndidzakuthandiza kutembenuza Isiraeli yense kukhala kumbali yako.”+