Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 31:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwo anadula mutu wa Sauli+ ndi kumuvula zida zake. Kenako anatumiza uthenga+ m’dziko lonse la Afilisiti, kunyumba za mafano awo+ ndi kwa anthu awo.

  • Salimo 115:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Manja ali nawo, koma sakhudza kanthu.+

      Mapazi ali nawo koma sayenda.+

      Satulutsa mawu ndi mmero wawo.+

  • Yesaya 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 M’tsiku limenelo, munthu wochokera kufumbi adzataya milungu yake yasiliva yopanda pake ndi milungu yake yagolide yopanda phindu, imene anthu anamupangira kuti aziigwadira. Adzaitayira kumene kumakhala aswiswiri* ndi mileme,+

  • Habakuku 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+

  • 1 Akorinto 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena