1 Samueli 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno anauza mtumiki wakeyo kuti: “Chonde, thamanga kuti ukatole mivi imene ndikuponya.”+ Mtumikiyo anathamanga, ndipo Yonatani anaponya muvi kuti upitirire mtumikiyo. 1 Samueli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo inam’kulira kwambiri Sauli, moti pamapeto pake oponya mivi ndi uta anamupeza ndipo anamuvulaza koopsa.+ 2 Samueli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uta wa Yonatani sunkalephera kupha adani ndi kukhetsa magazi awo,Sunkalephera kubaya mafuta a anthu amphamvu.+Lupanga la Sauli silinkabwerako chabe osakwaniritsa ntchito yake.+
36 Ndiyeno anauza mtumiki wakeyo kuti: “Chonde, thamanga kuti ukatole mivi imene ndikuponya.”+ Mtumikiyo anathamanga, ndipo Yonatani anaponya muvi kuti upitirire mtumikiyo.
3 Nkhondo inam’kulira kwambiri Sauli, moti pamapeto pake oponya mivi ndi uta anamupeza ndipo anamuvulaza koopsa.+
22 Uta wa Yonatani sunkalephera kupha adani ndi kukhetsa magazi awo,Sunkalephera kubaya mafuta a anthu amphamvu.+Lupanga la Sauli silinkabwerako chabe osakwaniritsa ntchito yake.+