Ekisodo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+ Deuteronomo 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwana wapathengo+ asalowe mumpingo wa Yehova. Ana ake asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10. Salimo 89:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ine ndidzawaimba mlandu ndi kuwalanga ndi ndodo,+Ndipo ndidzawalanga ndi zikoti chifukwa cha zolakwa zawo.+ Miyambo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+ ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+
2 “Mwana wapathengo+ asalowe mumpingo wa Yehova. Ana ake asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10.
32 Ine ndidzawaimba mlandu ndi kuwalanga ndi ndodo,+Ndipo ndidzawalanga ndi zikoti chifukwa cha zolakwa zawo.+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+