2 Samueli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno analowetsa likasa la Yehova muhema limene Davide anamanga n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako Davide anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+ Salimo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+
17 Ndiyeno analowetsa likasa la Yehova muhema limene Davide anamanga n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako Davide anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+
7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+