2 Samueli 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno mkaziyo anapitiriza kunena kuti: “N’chifukwa chiyani inu mfumu mwachitira+ anthu a Mulungu+ zinthu zowawononga? Popeza inu mfumu munapitikitsa+ mwana wanu, ndipo mwalephera kumuitanitsa, muli ndi mlandu+ pa zimene mwafotokozazi.
13 Ndiyeno mkaziyo anapitiriza kunena kuti: “N’chifukwa chiyani inu mfumu mwachitira+ anthu a Mulungu+ zinthu zowawononga? Popeza inu mfumu munapitikitsa+ mwana wanu, ndipo mwalephera kumuitanitsa, muli ndi mlandu+ pa zimene mwafotokozazi.