2 Samueli 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma mfumu inanena kuti: “Apite kunyumba kwake, koma asaone nkhope yanga.”+ Choncho Abisalomu anatembenukira kunyumba kwake, ndipo sanaonane ndi mfumu.
24 Koma mfumu inanena kuti: “Apite kunyumba kwake, koma asaone nkhope yanga.”+ Choncho Abisalomu anatembenukira kunyumba kwake, ndipo sanaonane ndi mfumu.