Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Poyankha azambawo anauza Farao kuti: “Amayi achiheberi sali ngati amayi achiiguputo. Popeza amayi achiheberi ndi amphamvu, mzamba asanafike iwo amakhala atabereka kale.”

  • Yoswa 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo amunawo atuluka usiku uno nthawi yotseka chipata+ itayandikira. Koma ine sindikudziwa kumene alowera. Fulumirani! Athamangireni! Muwapeza amenewo.”

  • 1 Samueli 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano Sauli anatuma amithenga kuti akagwire Davide, koma Mikala anati: “Akudwala.”+

  • 1 Samueli 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Davide anauza Ahimeleki wansembe kuti: “Mfumu yandituma nkhani inayake,+ ndipo yandiuza kuti, ‘Usauze munthu aliyense nkhani imene ndikukutuma ndi zimene ndakulamula.’ Choncho ndapangana ndi anyamata kuti ndikumane nawo pamalo enaake.

  • Mateyu 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena