-
Yoswa 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Chotero amuna aja anatuluka, nakafika kumapiri kuja. Anakhala kumeneko masiku atatu mpaka owasaka aja atabwerera. Owasakawo anawafunafuna mumsewu uliwonse, koma sanawapeze.
-