2 Samueli 22:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Iye amandichotsa pakati pa adani anga.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wochita zachiwawa.+ Salimo 55:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye adzandiwombola ndi kundikhazika pa mtendere, kundichotsa pankhondo,+Pakuti khamu la anthu landiukira.+ Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu wobwezera anthu oipa,+Inu Mulungu wobwezera anthu oipa, walani!+ Salimo 124:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova akanapanda kukhala kumbali yathu,+Pamene anthu anatiukira,+
49 Iye amandichotsa pakati pa adani anga.+Ndipo mudzandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mudzandilanditsa kwa munthu wochita zachiwawa.+
18 Iye adzandiwombola ndi kundikhazika pa mtendere, kundichotsa pankhondo,+Pakuti khamu la anthu landiukira.+