2 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Elisa anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene ndimam’tumikira,+ sindilandira.”+ Ndiyeno Namani anayamba kum’kakamiza kuti alandire, koma iye anakanabe. Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+
16 Koma Elisa anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene ndimam’tumikira,+ sindilandira.”+ Ndiyeno Namani anayamba kum’kakamiza kuti alandire, koma iye anakanabe.
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+