9 Koma pamene ndinasowa zofunika zina ndili kwanuko, sindinalemetse ngakhale munthu mmodzi,+ popeza abale amene anachokera ku Makedoniya+ anandipatsa zonse zimene ndinali kuzisowa. Ndithu, sindinakulemetseni m’njira iliyonse, ndipo ndipitirizabe kutero.+