Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 141:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Musachititse mtima wanga kukonda choipa chilichonse,+

      Kuti ndisamachite zinthu zoipa zonditchukitsa,+

      Pamodzi ndi amene amachita zinthu zopweteka anzawo,+

      Kuti ndisadye chakudya chawo chapamwamba.+

  • 1 Akorinto 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi.

  • Aefeso 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ndipo musamachite nawo+ ntchito zosapindulitsa za mu mdima.+ M’malomwake, muzidzudzula ntchitozo.+

  • 2 Yohane 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aliyense amene wamupatsa moni akugawana naye ntchito zake zoipazo.+

  • Chivumbulutso 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena