Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 M’mawa kutacha, Balamu anadzuka n’kumanga chishalo pabulu* wake, ndipo anapita limodzi ndi akalonga a ku Mowabu aja.+

  • Oweruza 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Inu okwera abulu ofiirira,+

      Inu okhala pansalu zokwera mtengo,

      Ndi inu oyenda mumsewu,

      Ganizirani ntchito za Mulungu izi:+

  • 2 Samueli 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Poyankha anati: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu+ ndinanena kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu wamkazi kuti ndikwerepo ndi kupita pamodzi ndi mfumu,’ pakuti ine mtumiki wanu ndine wolumala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena