Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+

  • 1 Samueli 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli anayamba kunena kuti: “N’chifukwa chiyani lero Yehova watigonjetsa pamaso pa Afilisiti?+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova+ ku Silo, kuti likhale pakati pathu ndi kutipulumutsa m’manja mwa adani athu.”

  • 1 Mafumu 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pa nthawi imeneyo, Yerobowamu anatuluka mu Yerusalemu, ndipo Ahiya+ Msilo+ yemwe anali mneneri, anam’peza panjira. Ahiya anali atavala chovala chatsopano. Awiriwo anali okhaokha kumeneko.

  • Yeremiya 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena