Salimo 89:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kodi pali mwamuna wamphamvu aliyense amene sadzaona imfa?+Kodi angathe kupulumutsa moyo wake m’dzanja la Manda?+ [Seʹlah.] Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
48 Kodi pali mwamuna wamphamvu aliyense amene sadzaona imfa?+Kodi angathe kupulumutsa moyo wake m’dzanja la Manda?+ [Seʹlah.]
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+