1 Mafumu 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye analamulira zaka zitatu ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Maaka,+ mdzukulu wa Abishalomu.*+ 2 Mbiri 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Rehobowamu anali kukonda kwambiri Maaka mdzukulu wa Abisalomu kuposa akazi ake ena onse+ ndi adzakazi* ake, pakuti iye anakwatira akazi 18, ndiponso anali ndi adzakazi 60. Iye anabereka ana aamuna 28 ndi ana aakazi 60.
2 Iye analamulira zaka zitatu ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Maaka,+ mdzukulu wa Abishalomu.*+
21 Rehobowamu anali kukonda kwambiri Maaka mdzukulu wa Abisalomu kuposa akazi ake ena onse+ ndi adzakazi* ake, pakuti iye anakwatira akazi 18, ndiponso anali ndi adzakazi 60. Iye anabereka ana aamuna 28 ndi ana aakazi 60.