Miyambo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+ Miyambo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’kosayenera kwa mafumu iwe Lemueli, n’kosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,+ kapena kuti akuluakulu olemekezeka azinena kuti: “Kodi chakumwa choledzeretsa chili kuti?” Luka 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Koma samalani kuti mitima yanu isalemedwe ndi kudya kwambiri, kumwa kwambiri,+ ndi nkhawa+ za moyo, kuti tsikulo lingadzakufikireni modzidzimutsa+
20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+
4 N’kosayenera kwa mafumu iwe Lemueli, n’kosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,+ kapena kuti akuluakulu olemekezeka azinena kuti: “Kodi chakumwa choledzeretsa chili kuti?”
34 “Koma samalani kuti mitima yanu isalemedwe ndi kudya kwambiri, kumwa kwambiri,+ ndi nkhawa+ za moyo, kuti tsikulo lingadzakufikireni modzidzimutsa+