1 Mafumu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita,+ ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli, komanso chifukwa cha zinthu zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli zimene Yerobowamu anachita.+ Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita,+ ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli, komanso chifukwa cha zinthu zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli zimene Yerobowamu anachita.+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]