Ekisodo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ Yobu 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uone wodzikweza aliyense n’kumuchepetsa,+Ndipo oipa uwaponderezere pamalo pomwe alilipo. Yesaya 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wanena kuti, ‘Ndi mphamvu za dzanja langa ndiponso ndi nzeru zanga, ndidzachitapo kanthu+ chifukwa ndine wodziwa zinthu. Ndidzachotsa malire a mitundu ya anthu,+ ndipo zinthu zimene anasunga ndidzazilanda.+ Monga munthu wamphamvu, ndidzagwetsa anthu okhala mmenemo.+
9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+
13 Pakuti iye wanena kuti, ‘Ndi mphamvu za dzanja langa ndiponso ndi nzeru zanga, ndidzachitapo kanthu+ chifukwa ndine wodziwa zinthu. Ndidzachotsa malire a mitundu ya anthu,+ ndipo zinthu zimene anasunga ndidzazilanda.+ Monga munthu wamphamvu, ndidzagwetsa anthu okhala mmenemo.+