-
1 Mafumu 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ahabu anafunsa kuti: “Kudzera mwa ndani?” Mneneriyo anayankha kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kudzera mwa anyamata otumikira akalonga oyang’anira zigawo.’” Pomalizira Ahabu anafunsa kuti: “Ndani akayambitse nkhondoyo?” Mneneriyo anayankha kuti: “Inuyo!”
-