2 Mbiri 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inuyo mupite nokha ndipo limbani mtima kukamenya nkhondo.+ Mulungu woona angakuchititseni kugonja kwa adani anu, chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu zomuthandiza+ munthu kapena zom’chititsa kugonja.”+ Salimo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+ Salimo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+Yembekezera Yehova.+
8 Inuyo mupite nokha ndipo limbani mtima kukamenya nkhondo.+ Mulungu woona angakuchititseni kugonja kwa adani anu, chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu zomuthandiza+ munthu kapena zom’chititsa kugonja.”+
8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+