Ekisodo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ngati waweruzidwa kuti apereke dipo,* ayenera kulipira mtengo wonse wowombolera moyo wake umene amugamula.+ Miyambo 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Moyo wa munthu udzawomboledwa ndi chuma chake,+ koma munthu wosauka sadzudzulidwa.+
30 Ngati waweruzidwa kuti apereke dipo,* ayenera kulipira mtengo wonse wowombolera moyo wake umene amugamula.+